Psalms 104:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ochimwa aonongeke pa dziko lapansi, anthu oipa asakhaleponso. Tamanda Chauta, iwe mtima wanga. Tamanda Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ochimwa athedwe kudziko lapansi, ndi oipa asakhalenso. Yamika Yehova, moyo wanga. Aleluya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu ochimwa awonongeke pa dziko lapansi ndipo anthu oyipa asapezekenso. Tamanda Yehova, Iwe moyo wanga. Tamandani Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ocimwa athedwe ku dziko lapansi, Ndi oipa asakhalenso. Yamika Yehova, moyo wanga. Haleluya.