Psalms 104:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudaliphimba ndi nyanja yozama ngati ndi chovala, ndipo madzi adakwera mpaka pamwamba pa mapiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudalikuta ndi nyanja ngati ndi chovala; madzi anafikira pamwamba pa mapiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munaliphimba ndi nyanja yozama ngati chovala; madzi anayimirira pamwamba pa mapiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudalikuta ndi nyanja ngati ndi cobvala; Madzi anafikira pamwamba pa mapiri,