Psalms 104:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mapiri adatumphuka, zigwa zidatsika, mpaka kumene Inu mudaakonzeratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
anakwera m'mapiri, anatsikira m'zigwa, kufikira malo mudawakonzeratu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munamiza mapiri, iwo anatsikira ku zigwa kumalo kumene munawakonzera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anakwera m'mapiri, anatsikira m'zigwa, Kufikira malo mudawakonzeratu.