Psalms 105:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene anali anthu oŵerengeka, anthu osatchuka, ongokhala nawo m'dzikomo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pokhala iwo anthu owerengeka, inde, anthu pang'ono, ndi alendo m'mwemo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene iwo anali ngati anthu ochepa mʼchiwerengero, ochepa ndithu, ndiponso alendo mʼdzikolo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pokhala iwo anthu owerengeka, Inde, anthu pang'ono, ndi alendo m'mwemo;