Psalms 105:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
omangoyendayenda kuchokera ku mtundu wina wa anthu kupita ku mtundu wina, kuchokera ku ufumu wina kupita ku ufumu wina,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nayendayenda kuchokera mtundu wina kufikira mtundu wina, kuchokera ufumu wina kufikira anthu ena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ankayendayenda kuchoka ku mtundu wina wa anthu ndi kupita ku mtundu wina, kuchoka mu ufumu wina kupita ku wina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nayendayenda kucokera mtundu wina kufikira mtundu wina, Kucokera ufumu wina kufikira anthu ena.