Psalms 105:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Chauta adadzetsa njala m'dziko la Kanani ndi kuwononga chakudya chonse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaitana njala igwere dziko; anathyola mchirikizo wonse wa mkate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anabweretsa njala pa dziko ndipo anawononga chakudya chonse;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaitana njala igwere dziko; Anatyola mcirikizo wonse wa mkate.