Psalms 105:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mpaka zimene Yosefe adanena zija zidachitikadi. Mau a Chauta adatsimikiza kuti iye sadalakwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kufikira nyengo yakuchitika maneno ake; mau a Yehova anamuyesa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mpaka zimene Iye ananeneratu zitakwaniritsidwa, mpaka mawu a Yehova ataonetsa kuti Iye ananena zoona.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kufikira nyengo yakucitika maneno ace; Mau a Yehova anamuyesa.