Psalms 105:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mfumu idalamula kuti akammasule, wolamulira mitundu ya anthuyo adammasuladi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumuyo anatuma munthu nammasula; woweruza mitundu ya anthu anamtsegulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu inatuma munthu kukamumasula, wolamulira wa mitundu ya anthu anamasula iyeyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumuyo anatuma munthu nammasula; Woweruza mitundu ya anthu anamtsegulira.