Psalms 105:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamsandutsa mbuye wa nyumba yake, ndi wolamulira chuma chake chonse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anamuika akhale woyang'anira nyumba yake, ndi woweruza wa pa zake zonse:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anamuyika kukhala wolamulira nyumba yake, wolamulira zonse zimene iye anali nazo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anamuika akhale woyang'anira nyumba yace, Ndi woweruza wa pa zace zonse: