Psalms 105:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti azilangiza nduna zake monga momwe ankafunira, ndi kuŵaphunzitsa nzeru akuluakulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amange nduna zake iye mwini, alangize akulu ake adziwe nzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kulangiza ana a mfumu monga ankafunira ndi kuphunzitsa nzeru akuluakulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amange nduna zace iye mwini, Alangize akulu ace adziwe nzeru.