Psalms 105:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Israele adafika ku Ejipito. Yakobeyo adakhala nawo m'dziko la Hamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo Israele analowa m'Ejipito; ndi Yakobo anakhala mlendo m'dziko la Hamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Israeli analowa mu Igupto; Yakobo anakhala monga mlendo mʼdziko la Hamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo Israyeli analowa m'Aigupto; Ndi Yakobo anakhala mlendo m'dziko la Hamu.