Psalms 105:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalola kuti anthu ake achuluke, naŵasandutsa amphamvu kupambana adani ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anachulukitsatu mtundu wa anthu ake, nawapatsa mphamvu yoposa owasautsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anachulukitsa anthu ake; ndipo anachititsa kuti akhale ochuluka kwambiri kuposa adani awo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacurukitsatu mtundu wa anthu ace, Nawapatsa mphamvu yoposa owasautsa.