Psalms 105:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaumitsa mitima ya adaniwo kuti adane ndi anthu ake ndi kuŵapanganirana zaupandu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anasanduliza mitima yao, kuti adane nao anthu ake, kuti achite monyenga ndi atumiki ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
amene mitima yawo anayitembenuza kuti idane ndi anthu ake, kukonzera chiwembu atumiki ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anasanduliza mitima yao, kuti adane nao anthu ace, Kuti acite monyenga ndi atumiki ace.