Psalms 105:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adachita zizindikiro m'dzina lake pakati pa anthuwo, adachita ntchito zozizwitsa m'dziko la Hamu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anaika pakati pao zizindikiro zake, ndi zodabwitsa m'dziko la Hamu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anachita zizindikiro zozizwitsa pakati pawo, zodabwitsa zake mʼdziko la Hamu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anaika pakati pao zizindikilo zace, Ndi zodabwiza m'dziko la Hamu.