Psalms 105:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adatumiza mdima, nasandutsa dzikolo kuti likhale lamdima. Komabe anthuwo adakaniratu mau a Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anatumiza mdima ndipo kunada; ndipo sanapikisane nao mau ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anatumiza mdima nasandutsa dziko kuti likhale la mdima. Koma anthuwo anakaniratu mawu a Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anatumiza mdima ndipo kunada; Ndipo sanapikisana nao mau ace.