Psalms 105:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adapha ana onse achisamba m'dziko mwao, ana onse oyamba, oŵabala akadali abiriŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Iye anapha achisamba onse m'dziko mwao, choyambira cha mphamvu yao yonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka anakantha ana onse oyamba kubadwa a mʼdziko lawo, zipatso zoyamba za umunthu wawo wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Iye anapha acisamba onse m'dziko mwao Coyambira ca mphamvu yao yonse.