Psalms 105:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Aejipito adasangalala pamene iwo adapita, chifukwa ankachita nawo mantha anthuwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ejipito anakondwera pakuchoka iwo; popeza kuopsa kwao kudawagwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko la Igupto linakondwa pamene iwo anachoka, pakuti kuopsa kwa Israeli kunawagwera iwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Aigupto anakondwera pakucoka iwo; Popeza kuopsa kwao kudawagwera.