Psalms 105:39 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adaika mtambo kuti uziphimba anthu ake, adaika moto kuti uziŵaunikira usiku.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anayala mtambo uwaphimbe; ndi moto uunikire usiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anatambasula mitambo ngati chofunda chawo, ndi moto owawunikira usiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anayala mtambo uwaphimbe; Ndi moto uunikire usiku,