Psalms 105:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵapatsa maiko a mitundu ina ya anthu, adalanda minda ya anthu ena kuti ikhale yao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawapatsa maiko a amitundu; iwo ndipo analanda zipatso za ntchito ya anthu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina ndipo anakhala olowamʼmalo a zimene ena anazivutikira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawapatsa maiko a amitundu; Iwo ndipo analanda zipatso za nchito ya anthu: