Psalms 105:45 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Potero Chauta adafuna kuti anthu ake azisunga malangizo ndi kumatsata malamulo ake onse. Tamandani Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti asamalire malemba ake, nasunge malamulo ake. Aleluya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti iwo asunge malangizo ake ndi kutsatira malamulo ake. Tamandani Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti asamalire malemba ace, Nasunge malamulo ace. Haleluya.