Psalms 105:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
musaiŵale ntchito zodabwitsa ndi zozizwitsa zimene ankazichita, ndiponso m'mene ankaweruzira anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
inu mbeu za Abrahamu, mtumiki wake, inu ana a Yakobo, osankhika ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
inu zidzukulu za Abrahamu mtumiki wake, inu ana a Yakobo, osankhika ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu mbeu za Abrahamu, mtumiki wace, Inu ana a Yakobo, osankhika ace.