Psalms 105:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amasunga chipangano chake nthaŵi zonse, sangaiŵale lamulo limene adalipereka ku mibadwo yonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akumbukira chipangano chake kosatha, mauwo anawalamulira mibadwo zikwi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyo amakumbukira pangano lake kwamuyaya, mawu amene analamula kwa mibado yonse,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akumbukila cipangano cace kosatha, Mauwo anawalamulira mibadwo zikwi;