Psalms 106:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero adaŵapulumutsa kwa amaliwongo, naŵalanditsa ku mphamvu za adani ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawapulumutsa m'dzanja la iye amene anawada, nawaombola kudzanja la mdani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anawapulumutsa mʼdzanja la amaliwongo; anawawombola mʼdzanja la mdani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawapulumutsa m'dzanja la iye amene anawada, Nawaombola ku dzanja la mdani.