Psalms 106:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adapanga mwanawang'ombe ku Horebu, napembedza chifano chosungunula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anapanga mwanawang'ombe ku Horebu, nagwadira fano loyenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anapanga mwana wangʼombe pa Horebu ndi kulambira fano loyengedwa kuchokera ku chitsulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anapanga mwana wa ng'ombe ku Horebu, Nagwadira fano loyenga.