Psalms 106:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adasinthanitsa ulemerero wa Mulungu ndi chifano cha ng'ombe imene imadya udzu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mwemo anasintha ulemerero wao ndi fanizo la ng'ombe yakudya msipu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anasinthanitsa ulemerero wawo ndi fano la ngʼombe yayimuna imene imadya udzu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mwemo anasintha ulemerero wao Ndi fanizo la ng'ombe Yakudya msipu.