Psalms 106:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ntchito zodabwitsa m'dziko la Hamulo, ndiponso zinthu zoopsa ku Nyanja Yofiira kuja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
zodabwitsa m'dziko la Hamu, zoopsa ku Nyanja Yofiira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zozizwitsa mʼdziko la Hamu ndi machitidwe ake woopsa pa Nyanja Yofiira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zodabwiza m'dziko la Hamu, Zoopsa ku Nyanja Yofiira.