Psalms 106:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake adaŵauza kuti akadaŵaononga, pakadapanda Mose wosankhidwa wake kuima pamaso pake, ndi kuletsa mkwiyo wake kuti usaŵaononge.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero Iye adati awaononge, pakadapanda Mose wosankhika wake, kuima pamaso pake pogamukapo, kubweza ukali wake ungawaononge.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Iye anawawuza kuti adzawawononga, pakanapanda Mose, mtumiki wake wosankhidwa, kuyima pamaso pake, ndi kuletsa mkwiyo wake kuti usawawononge.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero Iye adati awaononge, Pakadapanda Mose wosankhika wace, kuima pamaso pace pagamukapo, Kubweza ukali wace ungawaononge,