Psalms 106:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndipo kuti adzamwaza zidzukulu zao pakati pa mitundu ina, ndi kuzibalalitsa m'maikom'maiko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kugwetsanso mbeu zao mwa amitundu, ndi kuwabalalitsa m'maiko maiko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuchititsa kuti zidzukulu zawo zifere pakati pa anthu a mitundu ina ndi kuwabalalitsa mʼdziko lonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kugwetsanso mbeu zao mwa amitundu, Ndi kuwabalalitsa m'maiko maiko.