Psalms 106:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo adampsetsa mtima kwambiri, kotero kuti Moseyo adalankhula mosalingalira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti anawawitsa mzimu wake, ndipo analankhula zosayenera ndi milomo yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti iwowo anawukira mzimu wa Mulungu, ndipo pa milomo ya Mose panatuluka mawu osayenera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anawawitsa mzimu wace, Ndipo analankhula zosayenera ndi milomo yace.