Psalms 106:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo sadaonongeretu mitundu ina ya anthu monga m'mene Chauta adaaŵalamulira,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sanaononga mitunduyo ya anthu, imene Yehova adawauza;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Aisraeliwo sanawononge mitundu ya anthu monga momwe Yehova anawalamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sanaononga mitunduyo ya anthu, Imene Mulungu adawauza;