Psalms 106:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
koma adasakanizana ndi mitundu inayo naphunzira kuchita zoipa zomwe anthu enawo ankachita.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma anasokonekerana nao amitundu, naphunzira ntchito zao:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anasakanizana ndi anthu a mitundu inayo ndi kuphunzira miyambo yawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anasokonekerana nao amitundu, Naphunzira nchito zao: