Psalms 106:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatumikira mafano ao amene adasanduka msampha kwa iwo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatumikira mafano ao, amene anawakhalira msampha:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anapembedza mafano awo, amene anakhala msampha kwa iwowo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatumikira mafano ao, Amene anawakhalira msampha: