Psalms 106:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapereka nsembe ana ao aamuna ndi aakazi kwa mizimu yoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapereka ana ao aamuna ndi aakazi nsembe ya kwa ziwanda,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapereka nsembe ana awo aamuna ndi ana awo aakazi kwa ziwanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapereka ana ao amuna ndi akazi nsembe ya kwa ziwanda,