Psalms 106:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakhetsa magazi osachimwa, magazi a ana ao aamuna ndi aakazi, amene adaŵapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani, choncho dzikolo adaliipitsa ndi imfa zimenezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nakhetsa mwazi wosachimwa, ndiwo mwazi wa ana ao aamuna ndi aakazi, amene anawaperekera nsembe mafano a Kanani; m'mwemo analidetsa dziko ndi mwaziwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anakhetsa magazi a anthu osalakwa, magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi, amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanaani, ndipo dziko linayipitsidwa ndi magazi awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nakhetsa mwazi wosacimwa, ndi wo mwazi wa ana ao amuna ndi akazi, Amene anawaperekera nsembe mafano a Kanani; M'mwemo analidetsa dziko ndi mwaziwo.