Psalms 106:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adadzidetsa ndi ntchito zao, nakhala osakhulupirika pa zochita zao ngati mkazi wachigololo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anadziipsa nazo ntchito zao, nachita chigololo nao machitidwe ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anadzidetsa okha ndi zimene anachita; ndi machitidwe awo amakhala ngati munthu wachigololo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anadziipsa nazo nchito zao, Nacita cigololo nao macitidwe ao.