Psalms 106:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta, mundikumbukire pamene mukukomera mtima anthu anu. Mundithandize pamene mukuŵapulumutsa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundikumbukire, Yehova, monga momwe muvomerezana ndi anthu anu; mundionetsa chipulumutso chanu:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mundikumbukire Yehova, pamene mukuonetsa kukoma mtima kwanu kwa anthu anu, bwerani mudzandithandize pamene mukuwapulumutsa iwo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundikumbukile, Yehova, monga momwe mubvomerezana ndi anthu anu; Mundionetsa cipulumutso canu: