Psalms 106:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono mkwiyo wa Chauta udayakira anthu ake, chifukwa adanyansidwa nawo anthu akewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Potero udayaka mkwiyo wa Yehova pa anthu ake, nanyansidwa Iye ndi cholowa chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Yehova anakwiya ndi anthu ake ndipo ananyansidwa ndi cholowa chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Potero udayaka mkwiyo wa Yehova pa anthu ace, Nanyansidwa Iye ndi colowa cace.