Psalms 106:41 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaŵapereka kwa mitundu ina ya anthu, kotero kuti amene ankadana nawo, ndiwo amene ankaŵalamulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawapereka m'manja a amitundu; ndipo odana nao anachita ufumu pa iwo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawapereka kwa anthu a mitundu ina, ndipo adani awo anawalamulira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawapereka m'manja a amitundu; Ndipo odana nao anacita ufumu pa iwo.