Psalms 106:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nthaŵi zambiri Iye ankaŵapulumutsa, koma iwo ankamuukirabe osaleka, namamira m'machimo ao,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iye anawalanditsa kawirikawiri; koma anapikisana ndi Iye mwa uphungu wao, ndi mphulupulu zao zinawafoketsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye ankawapulumutsa nthawi zambiri, koma iwo ankatsimikiza za kuwukira ndipo anawonongeka mʼmachimo awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iye anawalanditsa kawiri kawiri; Koma anapikisana ndi Iye mwa uphungu wao, Ndi mphulupulu zao zinawafoketsa,