Psalms 106:44 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Chauta adaŵathandiza pa mavuto ao pamene adamva kulira kwao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anapenya nsautso yao, pakumva kufuula kwao:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Iye anaona kuzunzika kwawo pamene anamva kulira kwawo;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anapenya nsautso yao, Pakumva kupfuula kwao: