Psalms 106:45 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakumbukira chipangano chake chifukwa cha kuŵakonda anthuwo, naleza mtima chifukwa cha kukula kwa chikondi chake chosasinthika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawakumbukira chipangano chake, naleza monga mwa kuchuluka kwa chifundo chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha iwo Iye anakumbukira pangano lake ndipo anawalezera mtima chifukwa cha kukula kwa chikondi chake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawakumbukila cipangano cace, Naleza monga mwa kucuruka kwa cifundo cace.