Psalms 106:46 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adafeŵetsa mitima ya adani onse amene adagwira anthu ake ukapolo, kuti aŵachitire chifundo anthu akewo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anawachitira kuti apeze nsoni pamaso pa onse amene adawamanga ndende.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anachititsa kuti amene anawagwira iwo ukapolo awamvere chisoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anawacitira kuti apeze nsoni Pamaso pa onse amene adawamanga ndende.