Psalms 106:48 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atamandike Chauta, Mulungu wa Aisraele, kuyambira muyaya mpaka muyaya. Anthu onse anene kuti, “Inde momwemo.” Tamandani Chauta!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala Yehova, Mulungu wa Israele, kuyambira kosayamba kufikira kosatha. Ndi anthu onse anene, Amen. Aleluya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Atamandike Yehova, Mulungu wa Israeli, Kuyambira muyaya mpaka muyaya. Anthu onse anene kuti, “Ameni!” Tamandani Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala Yehova, Mulungu wa Israyeli, Kuyambira kosayamba kufikira kosatha. Ndi anthu onse anene, Amen. Haleluya,