Psalms 106:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti ndiwone zokoma za osankhidwa anu, kuti ndigaŵane nawo chisangalalo cha mtundu wanu, kuti ndipeze ulemerero pamodzi ndi anthu anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuti ndione chokomacho cha osankhika anu, kuti ndikondwere nacho chikondwerero cha anthu anu, kuti ndidzitamandire pamodzi ndi cholowa chanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti ndidzasangalale ndi chuma cha anthu anu osankhika, kuti ndidzakhale nacho chimwemwe cha anthu anu ndi kukhala pamodzi ndi cholowa chanu pa kukutamandani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ndione cokomaco ca osankhika anu, Kuti ndikondwere naco cikondwerero ca anthu anu, Kuti ndidzitamandire pamodzi ndi colowa canu.