Psalms 106:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Iye adaŵapulumutsa malinga ndi ulemerero wa dzina lake, kuti aonetse mphamvu zake zazikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma anawapulumutsa chifukwa cha dzina lake, kuti adziwitse chimphamvu chake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe Iye anawapulumutsa chifukwa cha dzina lake, kuti aonetse mphamvu zake zazikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma anawapulumutsa cifukwa ca dzina lace, Kuti adziwitse cimphamvu cace.