Psalms 107:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti adaatsutsa mau a Mulungu, adaakana monyoza malangizo a Wopambanazonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza anapikisana nao mau a Mulungu, napeputsa uphungu wa Wam'mwambamwamba;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti iwowo anawukira mawu a Mulungu ndi kunyoza uphungu wa Wammwambamwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza anapikisana nao mau a Mulungu, Napeputsa uphungu wa Wam'mwambamwamba;