Psalms 107:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iye adaŵapsinja ndi ntchito yakalavulagaga, motero iwo adagwa pansi, popanda mmodzi woŵathandiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kotero kuti anagonjetsa mtima wao ndi chovuta; iwowa anakhumudwa koma panalibe mthandizi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kotero Iye anawapereka kuti agwire ntchito yakalavulagaga; anagwa pansi ndipo panalibe woti awathandize.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kotero kuti anagonjetsa mtima wao ndi cobvuta; Iwowa anakhumudwa koma panalibe mthandizi.