Psalms 107:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ena adadwala chifukwa cha njira zao zoipa, nazunzika chifukwa cha machimo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu opusa azunzika chifukwa cha zolakwa zao, ndi chifukwa cha mphulupulu zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ena anakhala zitsiru chifukwa cha njira zawo zowukira, ndipo anamva zowawa chifukwa cha mphulupulu zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu opusa azunzika cifukwa ca zolakwa zao, Ndi cifukwa ca mphulupulu zao.