Psalms 107:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sankafuna chakudya cha mtundu uliwonse, ndipo adayandikira ku zipata za imfa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wao unyansidwa nacho chakudya chilichonse; ndipo ayandikira zipata za imfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo ananyansidwa ndi chakudya chilichonse ndipo anafika pafupi ndi zipata za imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wao unyansidwa naco cakudya ciri conse; Ndipo ayandikira zipata za imfa.