Psalms 107:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ena adakayenda ku nyanja m'zombo, namachita malonda pa Nyanja yaikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo akutsikira kunyanja nalowa m'zombo, akuchita ntchito zao pa madzi aakulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ena anayenda pa nyanja mʼsitima zapamadzi; Iwo anali anthu amalonda pa nyanja yayikulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo akutsikira kunyanja nalowa m'zombo, Akucita nchito zao pa madzi akuru;